Pitani ku nkhani yake

Zoti Muchite Pophunzira Baibulo

Pewani Mtima Wodzikuza

Nkhani yokhudza Davide, Abisalomu ndi Yowabu ingakuthandizeni kuti mudziwe kuopsa kokhala ndi mtima wodzikuza. Koperani nkhani ya m’Baibuloyi, iwerengeni, ndipo muiganizire mozama n’kuona mmene ingakuthandizireni.