Pitani ku nkhani yake

KODI BAIBULO LIMAPHUNZITSA CHIYANI?

Kodi Yesu Khristu Ndi Ndani? (Gawo 3)

Ganizirani makhalidwe ena amene Yesu anasonyeza ali padziko lapansi komanso mmene zimenezi zinasonyezera makhalidwe a Atate ake. Sindikizani nkhaniyi kenako muyankhe mafunsowo.