Pitani ku nkhani yake

KODI BAIBULO LIMAPHUNZITSA CHIYANI KWENIKWENI?

Ubatizo Umatithandiza Kuti Tikhale pa Ubwenzi ndi Mulungu (Gawo 3)

Nkhaniyi yachokera m’mutu 18 wa buku lakuti Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni?

Kodi ubatizo wachikhristu umatanthauza chiyani? Malinga ndi zimene Baibulo limanena, kodi Mkhristu amene wadzipereka kwa Mulungu ayenera kutani?