Pitani ku nkhani yake

KODI BAIBULO LIMAPHUNZITSA CHIYANI KWENIKWENI? (ZOKUTHANDIZANI POPHUNZIRA)

Pemphero Lingakuthandizeni Kukhala pa Ubwenzi ndi Mulungu (Gawo 1)

Zokuthandizani pophunzirazi zachokera m’buku lakuti Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni? mutu 17.

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zimene tingachite kuti Mulungu azimva mapemphero athu.