Pitani ku nkhani yake

KODI BAIBULO LIMAPHUNZITSA CHIYANI KWENIKWENI? (ZOKUTHANDIZANI POPHUNZIRA)

Khalani ndi Makhalidwe Amene Mulungu Amasangalala Nawo (Gawo 3)

Nkhaniyi yachokera m’mutu 12 m’buku lakuti Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani?

Pamafunika khama kuti tisintha makhalidwe athu n’kumatsatira mfundo za Mulungu. Koma kodi zimenezi n’zothandiza? Taganizirani zimene Baibulo limanena.