Pitani ku nkhani yake

KODI BAIBULO LIMAPHUNZITSA CHIYANI KWENIKWENI? (ZOKUTHANDIZANI POPHUNZIRA)

Yesetsani Kuti Muzilambira Mulungu M’njira Yovomerezeka (Gawo 2)

Zokuthandizani pophunzirazi zachokera m’mutu 16 wa buku lakuti Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni?

Kodi Akhristu ayenera kukakamiza anthu ena kuti ayambe kukhulupirira zimene iwowo amakhulupirira? Kodi mungafotokozere bwanji ena mosamala zimene mumakhulupirira?