Pitani ku nkhani yake

KODI BAIBULO LIMAPHUNZITSA CHIYANI KWENIKWENI? (ZOKUTHANDIZANI POPHUNZIRA)

Kulambira Kumene Mulungu Amavomereza (Gawo 1)

Zokuthandizani pophunzirazi zachokera m’mutu 15 wa buku lakuti Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni?

Kodi zipembedzo zonse zimasangalatsa Mulungu? Ngati si zonse, kodi mungatani kuti mudziwe chipembedzo choona?