Pitani ku nkhani yake

BAIBULO LIMAPHUNZITSA CHIYANI?

Kodi Ufumu wa Mulungu N’chiyani? (Gawo 2)

Kodi Ufumu wa Mulungu unachita kale zinthu ziti? Nanga kodi udzachita zotani m’tsogolo? Werengani kuti mudziwe zimene Baibulo limanena pankhaniyi.