Pitani ku nkhani yake

KODI BAIBULO LIMAPHUZITSA CHIYANI?

Dipo la Yesu Ndi Mphatso ya Mulungu Yamtengo Wapatali Kuposa Zonse (Gawo 2)

Werengani kuti mudziwe mmene dipo lingatithandizire ndiponso zimene tingachite posonyeza kuti timaliyamikira. Sindikizani kenako muyankhe mafunsowo.