Pitani ku nkhani yake

KODI BAIBULO LIMAPHUNZITSA CHIYANI KWENIKWENI? (ZOKUTHANDIZANI POPHUNZIRA)

Zimene Mungachite Kuti Banja Lanu Lizisangalala (Gawo 1)

Zokuthandizani pophunzirazi zachokera m’mutu 14 wa buku lakuti Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni?

Kodi chofunika kwambiri n’chiyani kuti banja likhale losangalala? Kodi malangizo a m’Baibulo angathandize bwanji amuna ndi akazi a pa banja?