Malo a pa webusaiti ya jw.org akuti “Pezani Malo Omwe Timasonkhana,” akonzedwanso. Tsopano mukhoza kufufuza zokhudza misonkhano ya mpingo, misonkhano yadera, komanso misonkhano yachigawo pamalo amodzi omwewo. Mukhozanso kuona malo osiyanasiyana pamapu, kuika malire a zinthu zomwe mungaone mukamafufuza zina zake, komanso kugwiritsa ntchito malowa mosavuta pachipangizo chanu cha m’manja.

Pitani pamalo a pa webusaiti akuti “Pezani Malo Omwe Timasonkhana.”