Pitani ku nkhani yake

ZATSOPANO

Mbali Yakuti: “Nkhani za M’mayiko”

Mbali Yakuti: “Nkhani za M’mayiko”

Pawebusaiti ya jw.org pawonjezeredwa mbali ina yakuti: “Nkhani za M’mayiko.” Mbali imeneyi izikhala ndi nkhani zomwe zili mu Buku Lapachaka lomwe langotuluka kumene. Nkhanizi zizikhala zofotokoza mmene ntchito komanso zinthu zina zokhudza Mboni za Yehova zikuyendera m’mayiko komanso m’madera osiyanasiyana. Pa mbali imeneyi pazikhalanso ziwerengero, zithunzi komanso malinki okuthandizani kutsegula nkhani zofotokoza mmene ntchito yathu ikuyendera padziko lonse.