Pitani ku nkhani yake

ZATSOPANO

Tsamba la Mavidiyo la pa JW.ORG Lakonzedwanso

Tsamba la Mavidiyo la pa JW.ORG Lakonzedwanso

Tsamba la mavidiyo pa jw.org lakonzedwanso ndipo tsopano:

  • Lili ndi mavidiyo onse a pa jw.org.

  • Mungafufuze mavidiyo.

  • Limasanja mavidiyo mofanana ndi mmene amasanjidwira pa JW Library komanso pa gawo la Mavidiyo Ena pa JW Broadcasting.

Mukhoza kupeza tsamba limene lakonzedwanso pogwiritsa ntchito tsamba lomwe lilipo kale, kuphatikizanso pamalo akuti, MABUKU > MAVIDIYO, Pezani Mavidiyo patsamba loyambirira la pa jw.org/ny komanso malo akuti Mavidiyo omwe amakhala pansi pa tsamba lililonse la jw.org/ny.

Onani tsamba la Mavidiyo lomwe lakonzedwanso.