Pitani ku nkhani yake

ZATSOPANO

M’kabuku ka Uthenga Wabwino Tsopano Muli Mavidiyo

M’kabuku ka Uthenga Wabwino Tsopano Muli Mavidiyo

M’kabuku ka Uthenga Wabwino Wochokera kwa Mulungu ka pa jw.org komanso pa JW Library tsopano muli mavidiyo omwe ali ndi mfundo zina zoonjezera. Ngati munapanga kale dawunilodi kabuku ka Uthenga Wabwino pa JW Library, pitani pa PUBLICATIONS > PENDING UPDATES kuti mupange dowunilodi kabuku katsopano komwe kali ndi mavidiyo.