Pitani ku nkhani yake

ZATSOPANO

Mafailo a MOBI Sazipezekanso pa Webusaiti Yathu

Mafailo a MOBI Sazipezekanso pa Webusaiti Yathu

Kuyambira pa October 3, 2016, tinasiya kuika mafailo a MOBI pa jw.org. Ngati muli ndi chipangizo chomwe chimagwiritsa ntchito Amazon Kindle, mungathe kupeza mabuku kapena magazini pogwiritsa ntchito imodzi mwa njira zomwe talemba m’munsimu:

  • Pangani dawunilodi zinthu pogwiritsa ntchito JW Library app. Pulogalamuyi ndi yaulere ndipo mungaipeze pa Amazon Appstore.

  • Pangani dawunilodi ma PDF a mabuku ndi zinthu zina pa jw.org. Ngati mumagwiritsa ntchito podikasiti ya Nsanja ya Olonda kapena Galamukani! ya MOBI, sankhani kuti magaziniwa azikhala a PDF. Gwiritsani ntchito linki ya MAPODIKASITI yomwe ikupezeka patsamba la MABUKU > MAGAZINI