Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

ZATSOPANO

Mayiko Ambiri Tsopano Akhoza Kupereka Zopereka Zawo Kudzera pa Intaneti

Mayiko Ambiri Tsopano Akhoza Kupereka Zopereka Zawo Kudzera pa Intaneti

Panopa mayiko ambiri akhoza kutumiza ndalama zothandizira ntchito yathu yolalikira padziko lonse komanso ntchito zina zimene timagwira pogwiritsa ntchito intaneti. Kuti mudziwe zimene mungachite potumiza ndalama ku dera lanu pitani pa tsamba lakuti, “Mmene Mungaperekere Ndalama Zothandizira Ntchito Yathu ya Padziko Lonse.”.