Pitani ku nkhani yake

ZATSOPANO

Pa JW Broadcasting Pawonjezeredwa Gawo Lofufuzira Zinthu

Pa JW Broadcasting Pawonjezeredwa Gawo Lofufuzira Zinthu

Ngati mumaonera JW Broadcasting pa intaneti kapena pa Amazon Fire TV, muona kuti tsopano paikidwa gawo lofufuzira zinthu. Gawoli lidzayamba kupezekanso pa Roku TV ndi Apple TV m’tsogolomu. Mungaonere pawebusaiti yathu kavidiyo kokuthandizani kudziwa mmene mungagwiritsire ntchito gawoli.