Panopa Buku Lachiwiri la Masalimo (Masalimo 42 mpaka 72) longomvetsera lochokera mu Baibulo la Dziko Latsopano lachingelezi lokonzedwanso laikidwa pa jw.org.

Mvetserani Buku Lachiwiri la Masalimo.