Panopa Buku la Nambala 5 la Masalimo (Masalimo 107 mpaka 150) longomvetsera lochokera mu Baibulo la Dziko Latsopano lachingelezi lokonzedwanso laikidwa pa jw.org.

Mvetserani Buku la Nambala 5 la Masalimo.