Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

ZATSOPANO

Baibulo Longomvetsera—Masalimo 1 Mpaka 41 Ayamba Kupezeka pa Intaneti

Baibulo Longomvetsera—Masalimo 1 Mpaka 41 Ayamba Kupezeka pa Intaneti

Panopa Buku Loyamba la Masalimo (Masalimo 1 mpaka 41) longomvetsera lochokera mu Baibulo la Dziko Latsopano lachingelezi lokonzedwanso laikidwa pa jw.org.

Mvetserani Buku Loyamba la Masalimo.