OCTOBER 5, 2020
ZATSOPANO
Pa JW.ORG Payamba Kupezeka Zokuthandizani Pogwiritsa Ntchito Amazon Alexa M’Chipwitikizi (cha ku Brazil)
Tsopano mungathe kumvetsera zinthu za pa jw.org pazipangizo zanu zomwe zili ndi Amazon Alexa m’Chipwitikizi (cha ku Brazil) pogwiritsa ntchito malangizo ochita kujambula.
Kuti mudziwe zambiri za mmene mungagwiritsire ntchito malangizo ochita kujambulawa pomvetsera zinthu za pa jw.org onani nkhani yakuti, “Use the JW.ORG Skill for Amazon Alexa.”

