Chichewa
Mabuku a 1 Atesalonika ndi 2 Atesalonika (Baibulo Lophunzirira) Akupezeka Panopa pa Intaneti
https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/500800020/univ/art/500800020_univ_sqr_xl.jpg

AUGUST 12, 2021
ZATSOPANO

Mabuku a 1 Atesalonika ndi 2 Atesalonika (Baibulo Lophunzirira) Akupezeka Panopa pa Intaneti

Mabuku a 1 Atesalonika ndi 2 Atesalonika (Baibulo Lophunzirira) Akupezeka Panopa pa Intaneti

Mabuku a 1 Atesalonika ndi 2 Atesalonika akupezeka panopa m’Baibulo Lophunzirira la Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika la Chingelezi pa jw.org. Mabukuwa ali ndi mfundo zothandiza pophunzira zokwana 150 komanso mavidiyo ndi zithunzi zambiri. Kuwonjezera pamenepa, mfundo zina zokhudza dzina la Mulungu m’Malemba a Chigiriki zawonjezedwa m’Zakumapeto C3 ndi C4.

Werengani mabuku a 1 Atesalonika ndi 2 Atesalonika.