AUGUST 15, 2019
ZATSOPANO

Buku la 1 Akorinto (Lothandiza Pophunzira) la Chingelezi Layamba Kupezeka pa Intaneti

Buku la 1 Akorinto (Lothandiza Pophunzira) la Chingelezi Layamba Kupezeka pa Intaneti

Buku la 1 Akorinto Lothandiza Pophunzira layamba kupezeka m’Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika pa jw.org m’chingelezi. Werengani notsi komanso onani zithunzi zomwe zikupezeka m’kachigawo ka zithunzi ndi mavidiyo. Komanso, m’kachigawo kameneka awonjezeramo zithunzi zatsopano za mabuku a Uthenga Wabwino ndi Machitidwe. Ku zakumapeto awonjezera mfundo zina zatsopano zokhudza dzina la Mulungu lakuti Yehova.

Werengani buku la 1 Akorinto.