Pitani ku nkhani yake

APRIL 15, 2019
ZATSOPANO

Baibulo la Dziko Latsopano Linatulutsidwa M’chijapanizi

Baibulo la Dziko Latsopano Linatulutsidwa M’chijapanizi

Pa 13 April, 2019, Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika lokonzedwanso linatulutsidwa mumzinda wa Kobe ku Japan. Baibulo la Dziko Latsopano lamasuliridwa lathunthu kapena mbali zake zina m’zinenero 179 kuphatikizapo m’zinenero 22 zomwe zakonzanso Mabaibulo awo mogwirizana ndi Baibulo lomwe linatulutsidwa mu 2013.