Pitani ku nkhani yake

SEPTEMBER 30, 2019
ZATSOPANO

Baibulo la Dziko Latsopano Latulutsidwa m’Chizapoteki (cha ku Isthmus)

Baibulo la Dziko Latsopano Latulutsidwa m’Chizapoteki (cha ku Isthmus)

Baibulo la Dziko Latsopano Lomasulira Malemba Achigiriki Achikhristu linatulutsidwa m’Chizapoteki (cha ku Isthmus) pa 27 September, 2019, ku Salina Cruz, Oaxaca, m’dziko la Mexico. Baibulo la Dziko Latsopano lamasuliridwa lathunthu kapena mbali zake zina m’ziyankhulo 185.