Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

AUGUST 15, 2012
UNITED STATES

Ku Manhattan Kwayambika Ntchito Yapadera

Ku Manhattan Kwayambika Ntchito Yapadera

Anthu ena a Mboni za Yehova ku Manhattan mumzinda wa New York, ayambitsa ntchito yapadera yogawira mabuku awo ofotokoza nkhani za m’Baibulo a m’zinenero zosiyanasiyana. Iwo akumaika mabukuwo pamatebulo omwe akumawaika m’malo osiyanasiyana ku Grand Central Station.