Pitani ku nkhani yake

21 JUNE, 2017
RUSSIA

Vidiyo Yosonyeza Apolisi ku Russia Akusokoneza Misonkhano ya Mboni za Yehova

Vidiyo Yosonyeza Apolisi ku Russia Akusokoneza Misonkhano ya Mboni za Yehova

Pa 25 May, 2017 apolisi ku Russia anasokoneza msonkhano umene a Mboni za Yehova ankachita mwamtendere mu mzinda wa Oryol.