Anthu a Mboni za Yehova akupitiriza kuthandiza anthu amene anapulumuka pa chivomezi chimene chinachitika ku Japan patapita chaka chimodzi chivomezichi chitachitika.