Japan

APRIL 29, 2016

Zivomezi ku Japan

NOVEMBER 26, 2014

A Mboni za Yehova Anathandiza Anthu Okhudzidwa ndi Kusefukira kwa Matope ku Hiroshima

Mvula yamphamvu yomwe inagwa ku Hiroshima, inachititsa kuti matope asefukire n’kupha anthu 74 ndipo anthu 1,600 anasowa pokhala. Ofesi ya Mboni za Yehova ya ku Japan nthawi yomweyo inapempha a Mboni ena kuti athandize pa ntchito yochotsa matope komanso zinyalala.

AUGUST 15, 2012

Timavidiyo: Japan: Moyo ukuyambiranso ku Japan patapita chaka chimodzi chivomezi chitachitika

Anthu a Mboni za Yehova akupitiriza kuthandiza anthu amene anapulumuka kutachitika chivomezi ndi madzi osefukira.