Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

SEPTEMBER 12, 2014
GERMANY

Kachigawo ka Vidiyo: A Mboni za Yehova Anapirira Nkhanza za Chipani cha Nazi

Kachigawo ka Vidiyo: A Mboni za Yehova Anapirira Nkhanza za Chipani cha Nazi

Nkhani yokhudza bambo August Dickmann omwe anaphedwa ku ndende ya Sachsenhausen, inafotokozedwa ndi anthu amene anaona ndi maso mmene anaphedwera. Anthuwa ndi bambo Josef Rehwald ndi a Heinrich Dickmann omwe anali achimwene awo a malemu August Dickmann.