Pitani ku nkhani yake

Germany

JULY 16, 2015

Bambo Wina ndi Mwana Wake Analandira Mendulo Yaulemu Chifukwa Chopulumutsa Anthu pa Ngozi ya Galimoto

A Andreas Bonk, omwe ndi a Mboni za Yehova, ndi mwana wawo Jorim analandira mendulo yaulemu chifukwa chakuti anachita zinthu molimba mtima komanso mosaganizira moyo wawo.

SEPTEMBER 12, 2014

Ku Sachsenhausen Kunachitika Mwambo Wokumbukira wa Mboni za Yehova Yemwe Anaphedwa ndi Chipani cha Nazi

Pa September 16, 2014, Bungwe la Brandenburg Memorials Foundation linachita mwambo wokumbukira kuti patha zaka 75 kuchokera pamene a August Dickmann anaphedwa kundende ya Sachsenhausen. Iwowa anali oyamba kuphedwa anthu ena akuona, pambuyo pa nkhondo yachiwiri ya padziko lonse ndi chipani cha Nazi chifukwa chokana kulowa usilikali potsatira zimene amakhulupirira.

APRIL 7, 2014

Bambo Richard Rudolph, Omwe Anapulumuka M’ndende Zozunzirako Anthu ku Germany, Amwalira Ali ndi Zaka 102

Bambo Richard Rudolph, omwe anali a Mboni za Yehova anamangidwa kwa zaka zoposa 19 chifukwa cha chikhulupiriro chawo.