Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

JULY 2, 2015
SOUTH KOREA

Kodi Dziko la South Korea Lidzasiya Liti Kuwatsekera M’ndende?

Kodi Dziko la South Korea Lidzasiya Liti Kuwatsekera M’ndende?

Pa zaka 60 zapitazi, dziko la South Korea linagamula kuti anyamata oposa 18,000, amene anakana usilikali chifukwa cha zimene amakhulupirira, akhale kundende. Tikaphatikiza zaka zonse zimene anyamatawa analamulidwa kuti akhale kundende zimakwana 35,000. Kodi ku South Korea anthu akusintha bwanji mmene amaonera nkhaniyi? Kodi dziko la South Korea lidzayamba liti kulemekeza ufulu wa anthu wokana usilikali chifukwa cha zimene amakhulupirira? Nanga kodi mayiko ena akuiona bwanji nkhaniyi? Vidiyoyi ikusonyeza chifukwa chake dziko la South Korea likuvutika kuchitapo kanthu pa nkhaniyi.