Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

ZOKHUDZA MALAMULO NDIPONSO UFULU WACHIBADWIDWE

Rwanda

JUNE 9, 2016

Boma la Rwanda Lathetsa Tsankho Limene Limachitika M’masukulu Chifukwa cha Kusiyana kwa Zipembedzo

Zimene boma lachita poteteza ufulu wopembedza umene ana a sukulu ali nawo ndi nkhani yosangalatsa kwambiri kwa ana a sukulu omwe ndi a Mboni.

MAY 6, 2016

Khothi Lalikulu Kwambiri Linachita Zinthu Mwachilungamo ku Rwanda

Ofesi yomva madandaulo a anthu m’dziko la Rwanda inauza Khoti Lalikulu Kwambiri kuti liunikenso chigamulo chake chokhudza Mboni za Yehova itazindikira kuti nkhaniyo sinayende mwachilungamo.