Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

DECEMBER 2, 2015
RUSSIA

Khoti la Taganrog Linapereka Chilango kwa a Mboni Chifukwa Chochita Zachipembedzo

Khoti la Taganrog Linapereka Chilango kwa a Mboni Chifukwa Chochita Zachipembedzo

Pa 30 November 2015, woweruza dzina lake Vasyutchenko wa kukhoti la ku Taganrog anagamula kuti a Mboni 16 ndi olakwa chifukwa chochita zachipembedzo. Koma kenako ananena kuti a Mboniwo asalipire chindapusa komanso kupita kundende pa nthawiyo. Kodi zimene anagamulazi zikukhudza bwanji anthu 16 amenewa? Nanga kodi zikukhudza bwanji a Mboni onse a ku Taganrog komanso m’madera ena a ku Russia? Vidiyoyi ikusonyeza zimene zinachitika kukhoti la ku Taganrog komanso mmene a Mboni za Yehova akuonera chigamulocho.