“Chinthu chokhacho chimene tinganene chokhudza a Mboni za Yehova pankhani ya chiwawa ndi choti a Mboniwo akhala akuchitiridwa zachiwawa.”

Katswiri wa Chikhalidwe cha Anthu Yemwenso Anali Woimira Bungwe Lina Lolimbana ndi Tsankho, Kuchitira Nkhanza Anthu a Kumayiko Ena ndi Kusalana