Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

ZOKHUDZA MALAMULO NDIPONSO UFULU WACHIBADWIDWE

Zokhudzana ndi Malamulo ku Russia

APRIL 4, 2017

Vasiliy Kalin: Zimene Woimira a Mboni Anayankhula Boma la Russia Litaopseza Kuti Liletsa Ntchito ya Mboni za Yehova M’dzikolo

Woimira Likulu la Mboni za Yehova m’dziko la Russia, a Vasiliy Kalin, akupempha akuluakulu a boma kuti asiye kuzunza a Mboni za Yehova popanda chifukwa.

APRIL 3, 2017

A Heiner Bielefeldt, Omwe Anali Nthumwi Yapadera ya Bungwe la United Nations pa Nkhani za Ufulu Wopembedza

“Ndikuganiza kuti ngati a Mboni za Yehova amachita zinthu zoopsa, ndiye kuti tonse timachita zinthu zoopsa.”