Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

PADZIKO LONSE

Mayiko Amene a Mboni za Yehova Akumangidwa Chifukwa Chotsatira Zimene Amakhulupirira

Mayiko Amene a Mboni za Yehova Akumangidwa Chifukwa Chotsatira Zimene Amakhulupirira

A Mboni za Yehova omwe amangidwa chifukwa cha chikhulupiriro chawo pofika mu January 2015

DZIKO

KUMANGIDWA

CHIFUKWA

Azerbaijan

1

  • Kukana kulowa usilikali chifukwa cha zimene amakhulupirira

Eritrea

64

  • Kukana kulowa usilikali chifukwa cha zimene amakhulupirira

  • Kuchita zinthu zokhudzana ndi chipembedzo chawo

  • Zifukwa zosadziwika bwinobwino

Korea, South

597

  • Kukana kulowa usilikali chifukwa cha zimene amakhulupirira

Nagorno-Karabakh

1

  • Kukana kulowa usilikali chifukwa cha zimene amakhulupirira

Singapore

19

  • Kukana kulowa usilikali chifukwa cha zimene amakhulupirira

Turkmenistan

2

  • Kukana kulowa usilikali chifukwa cha zimene amakhulupirira

Onse pamodzi

684

Gawo 18 lomwe lili m’Pangano la Dziko Lonse la Ufulu wa Anthu ndi wa Zandale * limanena kuti aliyense ali ndi “ufulu wonena maganizo ako, ufulu wotsatira zimene umakhulupirira ndiponso ufulu wopembedza.” M’mayiko ena a Mboni za Yehova akumamangidwa ndiponso kuchitidwa zinthu zankhanza kwambiri akamagwiritsa ntchito ufuluwu. Anthu a Mboni za Yehova ambiri amene akumangidwa ndi anyamata omwe akana kulowa usilikali chifukwa cha zimene amakhulupirira. Ndipo a Mboni ena akumamangidwa chifukwa chochita zimene amakhulupirira.

^ ndime 29 Onaninso zimene gawo 18 la chikalata cha mfundo za ufulu wachibadwidwe cha Universal Declaration of Human Rights limanena ndiponso gawo 9 la chikalata chotchedwa Pangano Lokhudza Ufulu wa Anthu ku Ulaya.