Akatswiri odziwa za ufulu wachibadwidwe ku Ulaya akukambirana nkhani yokhudza kukana kulowa usilikali, yomwe ikukhudzana ndi ufulu wachibadwidwe umene munthu aliyense ali nawo.

  • Bambo Nils Muiznieks omwe ndi Mkulu wa Bungwe Loona za Ufulu Wachibadwidwe wa anthu a m’mayiko a ku Ulaya, Bungweli linakhazikitsidwa kuti lizilimbikitsa  mayiko amene ali m’bungweli  kuti azilemekeza ufulu wa anthu.

  • Bambo Richard Clayton QC ndi oimira dziko la United Kingdom mu komiti yoona za malamulo ya Bungwe la mayiko a ku Ulaya.

Onerani zimene akatswiriwa ananena.