Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

ZOKHUDZA MALAMULO NDIPONSO UFULU WACHIBADWIDWE

Zokhudzana ndi Malamulo Padziko Lonse

MAY 12, 2014

Akatswiri Akufotokoza Zokhudza Ufulu Umene Munthu Ali Nawo, Wokana Kulowa Usilikali

Mayiko ambiri akuona kuti munthu ali ndi ufulu wokana kulowa usilikali. Mvetserani zimene akatswiri odziwa za ufulu wachibadwidwe akunena zoti nthawi yakwana yoti anthu padziko lonse ayambe kulemekeza ufulu wa anthu omwe akana kulowa usilikali.