Pitani ku nkhani yake

AUGUST 30, 2019
ERITREA

LIPOTI LAPADERA: A Mboni za Yehova Akuzunzidwa ku Eritrea

LIPOTI LAPADERA: A Mboni za Yehova Akuzunzidwa ku Eritrea

Lipoti lapaderali ndi lokhudza kuzunzidwa kwa a Mboni za Yehova ku Eritrea ndipo ndi la August 2019. Lipotili lakonzedwa ndi Dipatimenti Yoona Zofalitsa Nkhani kuti liperekedwe kwa akuluakulu a boma komanso kuti ligwiritsidwe ntchito pokambirana nawo.

Pangani Dawunilodi Lipoti la Chingelezi

Pofika mu August 2019, panali a Mboni za Yehova 52 omwe anali m’ndende ku Eritrea. Mndandanda wa mayinawu ulinso ndi zinthu zina zokhudza wa Mboni aliyense yemwe ali m’ndende.

Pangani Dawunilodi Mndandanda wa Chingelezi

Pa 28 April, 2018, bungwe la African Commission on Human and Peoples’ Rights (ACHPR) lomwe limaona za ufulu wa anthu m’mayiko a ku Africa, linaunika nkhani zokhudza nkhanza zomwe boma la Eritrea likuchitira a Mboni za Yehova. Kuyambira pa 24 October mpaka pa 13 November, 2018, bungwe la ACHPR linaunika mmene boma la Eritrea likuzunzira a Mboni za Yehova ndipo lipoti lotsatirali likufotokoza mwachidule zimene bungweli linapeza.

Pangani Dawunilodi Lipoti la Chingelezi