Pitani ku nkhani yake

Zokhudzana ndi Malamulo Komanso Ufulu Wachibadwidwe

 

RUSSIA

Vasiliy Kalin: Zimene Woimira a Mboni Anayankhula Boma la Russia Litaopseza Kuti Liletsa Ntchito ya Mboni za Yehova M’dzikolo

Woimira Likulu la Mboni za Yehova m’dziko la Russia, a Vasiliy Kalin, akupempha akuluakulu a boma kuti asiye kuzunza a Mboni za Yehova popanda chifukwa.

NAGORNO-KARABAKH

Mnyamata Wina ku Nagorno-Karabakh Anamangidwa Atakana Usilikali Chifukwa cha Zimene Amakhulupirira

Artur Avanesyan akugwira ukaidi wa miyezi 30 m’ndende ya Shushi ku Nagorno-Karabakh ngakhale kuti anali wokonzeka kugwira ntchito zina zomwe sizikhudza ndi usilikali.

ARMENIA

Gulu Loyamba la Mboni za Yehova ku Armenia Lamaliza Kugwira Ntchito Zimene Linapatsidwa Litakana Kulowa Usilikali

Panopo a Mboni ku Armenia angathe kugwira ntchito zimene sizikusemphana ndi zomwe amakhulupirira ndipo ntchitozo zimathandiza anthu ambiri.