Pitani ku nkhani yake

Zokhudzana ndi Malamulo Komanso Ufulu Wachibadwidwe

 

SOUTH KOREA

Akuvutika Chifukwa Chakuti Anakana Usilikali Potsatira Zomwe Amakhulupirira

Anthu omwe anakana kulowa usilikali ku South Korea, akupitiriza kuvutika ngakhale kuti anagwira kale ukaidi. Mbiri yoti anamangidwapo ikuchititsa kuti azikumana ndi mavuto osiyanasiyana.

SOUTH KOREA

Khoti la ku South Korea Lamva Madandaulo a Anthu Okana Usilikali

Khoti linagamula kuti likulu la asilikali lisiye kufalitsa pawebusaiti yawo mayina, ma adiresi komanso zinthu zina zokhudza anthu omwe amakana usilikali chifukwa cha zomwe amakhulupirira.

EGYPT

‘Ndikufunitsitsa Kudzaona Boma Litachotsa Chiletso Chomwe Linaikira a Mboni za Yehova’

Zaka zambirimbiri m’mbuyomo, a Mboni za Yehova ankapembedza mwaufulu ku Egypt. Nyuzi ina ya paintaneti inafotokoza kuti kuchokera nthawi imeneyo a Mboni za Yehova akhala akusonyeza makhalidwe abwino ngakhale kuti akhala akuzunzidwa kwa zaka zambiri.

SOUTH KOREA

Dziko la South Korea Likuchitira a Dong-hyuk Shin Zinthu Zopanda Chilungamo

Ufulu wa a Shin wochita zinthu mogwirizana ndi chikumbumtima chawo komanso chipembedzo chawo ukuphwanyidwa powalanga mopanda chilungamo chifukwa chokana kuchita maphunziro a ntchito ya usilikali.

GERMANY

Makhoti a ku Germany Amaona Misonkhano Ikuluikulu ya Mboni za Yehova Monga Maholide Achipembedzo

Misonkhano ya chigawo ya a Mboni tsopano imaonedwa monga maholide a chipembedzo, ndipo zimenezi zikusonyeza ufulu umene makolo ali nawo wophunzitsa ana awo zinthu zimene amakhulupirira.