Pitani ku nkhani yake

MAY 6, 2019
RUSSIA

Mmene a Dennis Christensen Anawamangira Komanso Kuwasunga M’ndende

Mmene a Dennis Christensen Anawamangira Komanso Kuwasunga M’ndende

Vidiyoyi ndi ya 11 minitsi ndipo ikusonyeza zomwe zakhala zikuchitika kungoyambira pamene a Dennis Christensen anamangidwa mu May 2017.