Russia

21 JULY, 2017

A Mboni za Yehova Ochokera M’mayiko Osiyanasiyana Analimbikitsa Abale Awo a ku Russia pa Nthawi Yozenga Mlandu wa Apilo

Bungwe Lolamulira linatumiza abale ochokera m’mayiko osiyanasiyana kupita ku Moscow.

MAY 28, 2020

Abale Athu Anasonyeza Chikhulupiriro Cholimba Atamenyedwa M’ndende ya ku Orenburg

M’vidiyoyi muli abale ochokera mumzinda wa Saratov ku Russia omwe anamangidwa komanso kuikidwa m’ndende chifukwa za zimene amakhulupirira. Alonda a ndende anamenya abalewa ndi zibonga. Chifukwa choti abalewa amadalira kwambiri Yehova, anapemphera ndipo anakwanitsa kupirira, kupeza mtendere ndi chimwemwe.