Pitani ku nkhani yake

Germany

JANUARY 10, 2019

Chionetsero Chokumbukira Nkhanza Zomwe a Mboni za Yehova Anakumana Nazo ku Germany

Chionetsero chomwe chikuchitika m’malo osiyanasiyana chikusonyeza kuti a Mboni za Yehova anazunzidwa ndi chipani cha Nazi komanso ulamuliro wa German Democratic Republic chifukwa cha chikhulupiriro chawo chomwe chinali champhamvu kwambiri.

SEPTEMBER 14, 2018

Chionetsero Chokumbukira Kuti Patha Zaka 70 Chichitikireni Msonkhano Wosaiwalika Chinachitika Mumzinda wa Kassel ku Germany

A Mboni za Yehova mumzinda wa Kassel anapanga chionetsero chokumbukira kuti patha zaka 70 chichitikireni msonkhano waukulu kwambiri womwe a Mboni anapanga pambuyo pa nkhondo yachiwiri yapadziko lonse.