Pitani ku nkhani yake

Nkhani Zokhudza Mboni za Yehova

Werengani nkhani zokhudza Mboni za Yehova pa intaneti. Palinso nkhani zothandiza akatswiri a zamalamulo komanso ofalitsa nkhani.

NKHANI ZA PADZIKO LONSE

A Mboni za Yehova Padziko Lonse Anasonyeza Mgwirizano pa Kampeni Yolembera Makalata Boma la Russia

Kampeni yolembera makalata akuluakulu a boma la Russia yomwe a Mboni anachita pofuna kuthandiza abale awo ndi umboni wochititsa chidwi wa kugwirizana kwa Mboni za Yehova padziko lonse.

MALAWI

Kampeni Yolemba Makalata M’malo mwa Abale Athu ku Russia—Kuchokera ku Malawi

A Mboni za Yehova ku Malawi akufotokoza zimene zinawachititsa kuti apange nawo kampeni yolemba makalata ya posachedwapa pofuna kuthandiza abale awo ku Russia.

UNITED STATES

Zomwe Zachitika pa Ntchito Yothandiza Anthu Omwe Anakhudzidwa ndi Mphepo Yamkuntho ya Harvey

Ntchito yothandiza a Mboni omwe anakhudzidwa ndi mphepoyi ikuyembekezereka kutha pofika mu June 2018.

MEXICO

A Mboni za Yehova Amtundu wa Huichol Anathamangitsidwa M’dera la Jalisco ku Mexico

Gulu la anthu linaukira a Mboni za Yehova n’kuwathamangitsa m’nyumba zawo. Abale anakadandaula nkhaniyi kwa akuluakulu a boma kuti awathandize.

NKHANI ZA PADZIKO LONSE

A Mboni Akugwira Mwakhama Ntchito Yothandiza Anthu Omwe Anakhudzidwa Ndi Mphepo Zamkuntho

Maofesi a Nthambi a Mboni za Yehova akufotokoza zimene akuchita pothandiza komanso kutonthoza mwauzimu anthu okhudzidwa ndi mphepo yamkuntho ya Irma ndi Maria.

UNITED STATES

Amboni a ku United States Anapirira Mavuto Obwera Chifukwa cha Mphepo ya Mkuntho Yotchedwa Hurricane Harvey

A Mboni za Yehova ambiri omwe nyumba zawo zinaonongeka chifukwa cha mphepo ya mkuntho akulandira thandizo kudzera mu dongosolo lomwe linapangidwa lothandizira anthuwa.

FINLAND

A Mboni za Yehova Akutonthoza Anthu Omwe Anakhudzidwa ndi Zauchifwamba ku Turku, Finland

Zimene ofesi ya nthambi inachita pothandiza mwamsanga anthu amene anakhudzidwa ndi zauchifwambazi zinathandiza kwambiri a Mboni komanso ena omwe si a Mboni.

MEXICO

A Mboni za Yehova ndi Okonzeka Kuyamba Ntchito Yomanganso Nyumba Zoonongeka ndi Chivomezi ku Guatemala ndi ku Mexico

A Mboni za Yehova ayamba ntchito yayikulu yothandiza a Mboni anzawo a ku Mexico ndi ku Guatemala amene anakhudzidwa ndi zivomezi ziwiri zomwe zinaononga kwambiri.