Pitani ku nkhani yake

2 DECEMBER, 2022
NKHANI ZA PADZIKO LONSE

Lipoti la Bungwe Lolamulira la Nambala 8 la 2022

Lipoti la Bungwe Lolamulira la Nambala 8 la 2022

Muvidiyoyi, m’bale wa m’Bungwe Lolamulira akutilimbikitsa kuti tizikhala okonzeka kusintha kuti tiziyenda limodzi ndi galeta la Yehova. Akutithandizanso kuona kufunika kochita misonkhano yapamasom’pamaso.