Pitani ku nkhani yake

28 OCTOBER, 2022
NKHANI ZA PADZIKO LONSE

Lipoti la Bungwe Lolamulira la Nambala 7 la 2022

Lipoti la Bungwe Lolamulira la Nambala 7 la 2022

M’bale wa m’Bungwe Lolamulira akufotokoza malipoti okhudza zinthu zimene tayambiranso kuchita pamasom’pamaso komanso okhudza zimene tikuchita pantchito yothandiza abale amene akumana ndi mavuto. Akutilimbikitsanso kuti tizichitapo kanthu mwamsanga tikaona tsoka.