Pitani ku nkhani yake

Nkhani Zimene Zapezeka Posachedwapa Patsamba Loyamba

 

Kodi Moyo Udzabwereranso Mwakale?

Kodi Baibulo limati chiyani pa nkhaniyi?

 

Kodi Baibulo Limati Chiyani pa Nkhani ya Miliri?

Anthu ena amanena kuti Mulungu akugwiritsa ntchito miliri ndi matenda ena polanga anthu masiku ano. Koma zimenezi n’zosagwirizana ndi zimene Baibulo limanena.

Zimene Zingakuthandizeni Ngati Mwayamba Kudwala Mwadzidzidzi

Kodi ndi mfundo ziti za m’Baibulo zimene zingakuthandizeni ngati mwayamba kudwala mosayembekezereka?

Kodi “Alefa ndi Omega ndi Ndani”?

N’chifukwa chiyani dzina limeneli ndi loyenera?

Kodi Tingapewe Bwanji Matenda?

Matenda akale komanso amene angoyamba kumene akhoza kusokoneza thanzi lanu. Kodi mungadziteteze bwanji?

Kodi Zipembedzo Zonse N’zofanana Ndipo Zimathandizadi Anthu Kudziwa Mulungu?

Mfundo ziwiri zofotokozedwa m’Baibulo zingatithandize kudziwa yankho la funsoli.

Zimene Mungachite Ngati Mukupeza Ndalama Zochepa

Mavuto azachuma akabwera mwadzidzidzi zimadetsa nkhawa, koma mfundo za m’Baibulo zingakuthandizeni kuti muzitha kugwiritsa ntchito ndalama zochepa.

Kodi Nkhondo ya Aramagedo Idzakhala Yotani?

Mawu akuti Aramagedo amapezeka kamodzi kokha m’Baibulo, koma nkhondo imene mawuwa amatanthauza imatchulidwa m’Baibulo lonse.

Zimene Mungachite Kuti Muzisangalala Kwambiri Masiku Ano

Munkhanizi tiona zinthu 6 zimene zingakuthandizeni kuti muzikhala okhutira komanso kuti muzisangalala kwambiri masiku ano.