Kupirira Mavuto

A Mboni za Yehova amakhalabe achimwemwe ndiponso okhutira ngakhale atakhala ndi matenda komanso vuto la kulumala.

Amalimbikitsa Ena Ngakhale Kuti Akudwala

Posafuna kumangokhalira kudzimvera chisoni, Clodean anapemphera kwa Mulungu kuti amupatse mphamvu zoti azitha kulimbikitsa anthu ena.

Kutumikira Mulungu Kuli Ngati Mankhwala Ake

Onesmus anabadwa ndi matenda a mafupa. Onani mmene malonjezo a m’Baibulo amulimbikitsira

Kuyandikira kwa Mulungu Ndi Kwabwino

Sarah Maiga anasiya kukula ali ndi zaka 9 koma akutumikira Yehova mwakhama.

Yehova Anandithandiza pa Nthawi Yomwe Ndinkafunikiradi Kuthandizidwa

Ali ndi zaka 20, Miklós Aleksza analumala atachita ngozi. Kodi Baibulo linamuthandiza bwanji kukhala ndi chiyembekezo?

“Ngati Kingsley Akukwanitsa, Kuli Bwanji Ine?”

Kingsley wa ku Sri Lanka anali ndi mavuto aakulu koma anachita khama kwambiri kuti akwanitse kuwerenga Baibulo kwa maminitsi ochepa.

Wosaona Ndiponso Wosamva

James Ryan anabadwa ndi vuto losamva ndipo kenako anakhalanso ndi vuto losaona. Kodi n’chiyani chinamuthandiza kudziwa cholinga cha moyo?

“Ndimayesetsa Kuti Ndisamangoganizira za Matenda Anga”

N’chiyani chimathandiza Elisa kupirira komanso kuiwalako matenda ake?

Sanasiye Kutsatira Zimene Amakhulupirira

Song Hee Kang anakhala wokhulupirika pamene anadwala kwambiri ali ndi zaka 14.